1 Samuel 28:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Saulo ataona gulu laankhondo la Afilisti, adayamba kuwopa ndi kunjenjemera kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene Saulo anaona khamu la Afilisti, anaopa, ndi mtima wake unanjenjemera kwakukulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sauli ataona gulu lankhondo la Afilisti anaopa ndipo ananjenjemera kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene Sauli anaona khamu la Afilisti, anaopa, ndi mtima wace unanjenjemera kwakukuru.