1 Samuel 29:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ameneyutu ndi Davide, yemwe uja ankamuvinira ndi kumuimbira kuti, “ ‘Saulo wapha zikwi inde, koma Davide wapha zikwi khumikhumi?’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Uyu si Davide kodi amene anamthirirana mang'ombe m'magulu ao, kuti, Saulo anapha zikwi zake, koma Davide zikwi zake zankhani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Paja ameneyu ndi Davide yemwe ankamuvinira namuyimbira kuti, “ ‘Sauli wapha anthu 1,000 koma Davide wapha miyandamiyanda?’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Uyu si Davide kodi amene anamthirirana mang'ombe m'magulu ao, kuti, Sauli anapha zikwi zace, Koma Davide zikwi zace zankhani?