1 Samuel 3:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Eli adamuitana nati, “Samuele mwana wanga.” Samuele adati, “Ŵaŵa!”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Eli anaitana Samuele, nati, Mwana wanga, Samuele. Nati iye, Ndine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Eli anamuyitana nati, “Samueli mwana wanga.” Samueli anayankha kuti, “Wawa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Eli anaitana Samueli, nati, Mwana wanga, Samueli. Nati iye, Ndine.