1 Samuel 3:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monse Samuele ankakula, Chauta anali naye, motero zonse zimene Samueleyo ankanena zinkachitikadi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Samuele anakula, Yehova nakhala naye, osalola kuti mau ake amodzi apite pachabe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anali ndi Samueli pamene amakula, ndipo zonse zimene ankayankhula zinkachitikadi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Samueli anakula, Yehova nakhala naye, osalola kuti mau ace amodzi apite pacabe.