1 Samuel 30:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Davide adagamula kuti njira imeneyi ikhale lamulo lokhazikika pakati pa Aisraele, kuyambira tsiku limenelo mpaka pano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kuyambira tsiku lija kufikira lero lomwe anaika ichi, chikhale lemba ndi chiweruzo pa Aisraele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Davide anakhazikitsa ngati lamulo mʼchitidwe woterewu pakati pa Aisraeli kuyambira tsiku limenelo mpaka lero.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kuyambira tsiku lija kufikira lero lomwe anaika ici, cikhale lemba ndi ciweruzo pa Aisrayeli.