1 Samuel 30:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Davide atafika ku Zikilagi, adapatulako zofunkha kusungira abwenzi ake, atsogoleri a ku Yuda, nauza aliyense kuti, “Nayi mphatso yanu yotapa pa zolanda kwa adani a Chauta.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene Davide anafika ku Zikilagi, anatumizako za zofunkhazo kwa akulu a Yuda, ndiwo abwenzi ake, nati, Siyi mphatso yanu ya zofunkha za adani a Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide atafika ku Zikilagi, anatumiza zina mwa zofunkhazo kwa akuluakulu a Yuda, amene anali abwenzi ake. Anati, “Nayi mphatso yanu yochokera pa zofunkha za adani a Yehova.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene Davide anafika ku Zikilaga, anatumizako za zofunkhazo kwa akuru a Yuda, ndiwo abwenzi ace, nati, Siyi mphatso yanu ya zofunkha za adani a Yehova.