1 Samuel 30:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mphatsozo zidaperekedwa kwa anthu a ku Betele, a ku Ramoti kumwera kwa Yuda, a ku Yatiri,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anatumiza kwa iwo a ku Betele, ndi kwa iwo a ku Ramoti wa kumwera, ndi kwa iwo a ku Yatiri;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anatumiza mphatsozo kwa anthu a ku Beteli, Ramoti-Negavi, Yatiri,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anatumiza kwa iwo a ku Beteli, ndi kwa iwo a ku Ramoti wa kumwela, ndi kwa iwo a ku Yatiri;