1 Samuel 30:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
a ku Rakala, a ku mizinda ya fuko la Ayeramiyele, a ku mizinda ya fuko la Akeni,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kwa iwo a ku Rakala, ndi kwa iwo a ku m'midzi ya Ayerameele, ndi kwa iwo a m'midzi ya Akeni;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Rakala, mizinda ya fuko la Ayerahimeeli, mizinda ya fuko la Akeni,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kwa iwo a ku Rakala, ndi kwa iwo a m'midzi ya Ayerameli, ndi kwa iwo a m'midzi ya Akeni;