1 Samuel 30:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Davide ndi anthu ake adalira mokweza, mpaka mphamvu zolirira zidaŵathera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide ndi anthu amene anali naye anakweza mau ao, nalira misozi, kufikira analibe mphamvu yakuliranso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero Davide ndi anthu ake analira mofuwula mpaka analibenso mphamvu zolirira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide ndi anthu amene anali naye anakweza mau ao, nalira misozi, kufikira analibe mphamvu yakuliranso.