1 Samuel 30:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nawonso akazi a Davide anali atatengedwa ukapolo. Maina ao anali Ahinowamu wa ku Yezireele ndi Abigaile mkazi wamasiye wa Nabala wa ku Karimele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo akazi awiri a Davide anatengedwa ukapolo, Ahinowamu wa ku Yezireele ndi Abigaile mkazi wa Nabala wa ku Karimele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akazi awiri a Davide, Ahinoamu wa ku Yezireeli ndi Abigayeli mkazi wa Nabala wa ku Karimeli anatengedwanso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo akazi awiri a Davide anatengedwa ukapolo, Ahinoamu wa ku Jezreeli ndi Abigayeli mkazi wa Nabala wa ku Karimeli.