1 Samuel 31:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adaika zida zankhondo za Sauloyo m'nyumba yopembedzeramo Asitaroti, mulungu wao. Ndipo adakhomerera mtembo wake ku khoma la mzinda wa Betisani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaika zida zake m'nyumba ya Asitaroti; napachika mtembo wake ku linga la ku Beteseani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anayika zida zake zankhondo mʼnyumba yopembedzera Asitoreti, ndipo thupi lake analikhomera pa khoma la mzinda wa Beti-Sani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaika zida zace m'nyumba ya Asitarote; napacika mtembo wace ku linga la ku Betisani.