1 Samuel 6:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵiyo anthu a ku Betesemesi ankadula tirigu m'chigwa. Ndipo pamene adati tha, napenya Bokosi lachipanganolo likubwera, adakondwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo a ku Betesemesi analikumweta tirigu wao m'chigwamo; natukula maso ao, naona likasalo, nakondwera pakuliona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawi imeneyi anthu a ku Beti-Semesi amakolola tirigu mʼchigwa ndipo pamene anayangʼana ndi kuona Bokosi la Chipangano likubwera anakondwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo a ku Betisemesi analikumweta tirigu wao m'cigwamo; natukula maso ao, naona likasalo, nakondwerapakuliona.