1 Samuel 6:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Afilisti adaitana ansembe ao ndi anthu amaula naŵafunsa kuti, “Tichite nalo chiyani Bokosi lachipanganoli? Tiwuzeni. Kodi Bokosi limeneli tingalibwezere ku malo ake mwa njira yanji?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Afilistiwo anaitana ansembe ndi oombeza, nati, Tichitenji ndi likasa la Yehova? Mutidziwitse chimene tilitumize nacho kumalo kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Afilisti anayitana ansembe ndi amawula ndipo anati, “Tichite nalo chiyani Bokosi la Yehova? Tiwuzeni momwe tidzalitumizira ku malo ake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Afilistiwo anaitana ansembe ndi oombeza, nati, Ticitenji ndi likasa la Yehova? mutidziwitse cimene tilitumize naco kumalo kwace.