1 Samuel 8:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Idzakulandani minda yanu yabwino kwambiri, minda yanu yamphesa ndi yaolivi, kudzanso minda yanu yazipatso, ndi kuipatsa nduna zake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo idzalanda minda yanu, ndi minda ya mphesa yanu, ndi minda ya azitona, inde minda yoposayo, nidzaipatsa anyamata ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Idzatenga minda yanu yabwino ya mpesa ndi ya mitengo ya olivi ndipo adzayipereka kwa antchito ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo idzalanda minda yanu, ndi minda yamphesa yanu, ndi minda yaazitona, inde minda yoposayo, nidzaipatsa anyamata ace.