1 Samuel 8:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Idzalanda gawo lachikhumi la tirigu wanu ndi la mphesa zanu, nidzapatsa kwa akapitao ake ndi nduna zake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo idzatenga limodzi la magawo khumi la mbeu zanu, ndi la minda yanu yamphesa, nidzalipatsa akapitao ake, ndi anyamata ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Idzatenga gawo lakhumi la tirigu wanu ndi mphesa zanu ndi kupereka kwa nduna zake ndi akapitawo ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo idzatenga limodzi la magawo khumi la mbeu zanu, ndi la minda yanu yamphesa, nidzalipatsa akapitao ace, ndi anyamata ace.