1 Samuel 8:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthuwo adakana kumvera mau a Samuele. Adati, “Iyai! Ife tikufuna mfumu yotilamulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anthu anakana kumvera mau a Samuele; nati, Iai, koma tifuna kukhala nayo mfumu yathu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma anthu anakana kumumvera Samueli. Iwo anati, “Ayi! Ife tikufuna mfumu yotilamulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anthu anakana kumvera mau a Samueli; nati, Iai, koma tifuna kukhala nayo mfumu yathu;