1 Samuel 8:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tikufuna kuti nafenso tikhale ngati mitundu ina yonse, ndipo kuti mfumu yathu izitiweruza, kutitsogolera ndi kumatimenyera nkhondo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti ifenso tikafanane nao anthu a mitundu yonse; kuti mfumu yathuyo ikatiweruzire, ndi kutuluka kutitsogolera, ndi kuponya nafe nkhondo zathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero ifenso tidzakhala ngati mayiko ena. Mfumu yathu idzatiweruza ndiponso idzatuluka nafe kutitsogolera kukamenya nkhondo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti ifenso tikafanane nao anthu a mitundu yonse; kuti mfumu yathuyo ikatiweruzire, ndi kuturuka kutitsogolera, ndi kuponya nafe nkhondo zathu.