1 Samuel 9:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene ankakwera phiri kupita kumzindako, adakumana ndi atsikana akutuluka mumzindamo kukatunga madzi, ndipo adaŵafunsa kuti, “Kodi mlosi uja alipo?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakukwera kumudziko anapeza anthu akazi alikutuluka kuti akatunge madzi, nanena nao, Mlauliyo alipo kodi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akukwera phiri kupita ku mzindawo anakumana ndi atsikana akutuluka mu mzindamo kukatunga madzi, ndipo anawafunsa kuti, “Kodi mlosi uja alipo?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakukwera kumudziko anapeza anthu akazi alikuturuka kuti akatunge madzi, nanena nao, Mlauliyo alipo kodi?