1 Samuel 9:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho adapita kumzindako. Poloŵa mumzindamo, adaona Samuele akutuluka kumene, alikudza kwa iwo pa njira yopita kukachisi kuja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwowa anakwera kumudzi; ndipo m'mene analowa m'mudzimo, onani, Samuele anatulukira pali iwo, kuti akakwere kumsanje.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho anapita ku mzinda kuja. Akulowa mu mzindamo, anaona Samueli akutuluka mu mzindamo akubwera kumene kunali iwo, koma amapita ku phiri, ku malo wopatulika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwowa anakwera kumudzi; ndipo m'mene analowa m'mudzimo, onani, Samueli anaturukira pali Iwo, kuti akakwere kumsanje.