1 Samuel 9:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Samuele ataona Saulo, Chauta adamuuza kuti, “Ndi ameneyu munthu ndidakuuza uja. Ndiye amene adzalamulire anthu anga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene Samuele anaona Saulo, Yehova anati kwa iye, Ona munthu amene ndinakuuza za iye! Ameneyu adzaweruza anthu anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Samueli atamuona Sauli, Yehova anamuwuza kuti, “Munthu ndinakuwuza uja ndi uyu. Iyeyu adzalamulira anthu anga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene Samueli anaona Sauli, Yehova anati kwa iye, Ona munthu amene ndinakuuza za iye! ameneyu adzaweruza anthu anga.