1 Samuel 9:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Saulo adayandikira Samueleyo ku chipata namufunsa kuti, “Zikomo, kodi kunyumba kwa mlosi nkuti?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pomwepo Saulo anayandikira kwa Samuele pakati pa chipata, nati, Mundidziwitse nyumba ya mlauliyo ili kuti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Sauli anayandikira Samueli pa chipata ndipo anamufunsa, “Kodi mungandiwuze kumene kuli nyumba ya mlosi?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pomwepo Sauli anayandikira kwa Samueli pakati pa cipata, nati, Mundidziwitse nyumba ya mlauliyo iri kuti.