1 Samuel 9:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Samuele adamuyankha kuti, “Mlosiyo ndine. Tsogolaniko ku kachisi, poti lero mudya nane, ndipo m'maŵa ndikuuzani zonse zimene zili mumtima mwanu, kenaka ndidzakulolani kuti mupite.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Samuele anayankha Saulo nati, Ine ndine mlauliyo. Kwera, batsogola kumsanje, pakuti mudzadya ndi ine lero; ndipo m'mawa ndidzakulola upite, ndi kukudziwitsa zonse zili mumtima mwako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Samueli anayankha, “Ine ndine mlosiyo. Tsogolani kupita ku phiri pakuti lero mudya ndi ine, ndipo mawa mmawa ndidzakuwuzani zonse zimene zili mu mtima mwanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Samueli anayankha Sauli nati, Inendinemlauliyo. Kwera, batsogola kumsanje, pakuti mudzadya ndi ine lero; ndipo m'mawa ndidzakulola upite, ndi kukudziwitsa zonse ziri mumtima mwako.