1 Samuel 9:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iyeyo anali ndi mwana dzina lake Saulo, mnyamata wokongola. Pakati pa Aisraele onse panalibenso mnyamata wokongola kupambana iyeyo. Anali wamtali kotero kuti anthu ena onse ankamugwa m'mapewa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye anali ndi mwana wamwamuna dzina lake Saulo, mnyamata wokongola; pakati pa anthu onse a Israele panalibe wina wokongola ngati iye; anali wamtali, anthu onse ena anamlekeza m'chifuwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iyeyu anali ndi mwana dzina lake Sauli, mnyamata wa maonekedwe abwino. Pakati pa Aisraeli onse panalibe wofanana naye. Anali wamtali kotero kuti anthu onse ankamulekeza mʼmapewa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye anali ndi mwana wamwamuna dzina lace Sauli, mnyamata wokongola; pakati pa anthu onse a Israyeli panalibe wina wokongola ngati iye; anali wamtali, anthu onse ena anamlekeza m'cifuwa.