1 Samuel 9:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Samuele adatenga Saulo ndi mnyamata wake uja, ndipo adaloŵa nawo m'chipinda chachikulu, naŵapatsa malo kutsogolo kwa anthu oitanidwa, amene onse pamodzi anali ngati anthu makumi atatu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Samuele anatenga Saulo ndi mnyamata wake, napita nao ku chipinda cha alendo, nawakhalitsa pa malo a ulemu pakati pa oitanidwa onse; ndiwo anthu monga makumi atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Samueli anatenga Sauli ndi mnyamata wake uja ndi kulowa nawo mʼchipinda chachikulu ndipo anawakhazika kutsogolo kwa anthu oyitanidwa. Onse pamodzi analipo anthu makumi atatu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Samueli anatenga Sauli ndi mnyamata wace, napita nao ku cipinda ca alendo, nawakhalitsa pa malo a ulemu pakati pa oitanidwa onse; ndiwo anthu monga makumi atatu.