1 Samuel 9:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adauza wophika kuti, “Bwera nayo nthuli yanyama ija ndidaakupatsayi. Paja ndidaakuuza kuti uiike pambali.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Samuele ananena ndi wophika, Tenga nyama ndinakupatsa, ndi kuti, Ibakhala ndi iwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Samueli anati kwa wophika, “Bwera nayo nyama imene ndinakupatsa, imene ndinakuwuza kuti uyisunge pambali.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Samueli ananena ndi wophika, Tenga nyama ndinakupatsa, ndi kuti, Ibakhala ndi iwe.