1 Thessalonians 1:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Abale athu, inu amene Mulungu amakukondani, tikudziŵa kuti Iye adakusankhani kuti mukhale ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
podziwa, abale okondedwa ndi Mulungu, chisankhidwe chanu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abale okondedwa ndi Mulungu, tikudziwa kuti Mulungu anakusankhani,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
podziwa, abale okondedwa ndi Mulungu, cisankhidwe canu,