1 Thessalonians 1:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero nanunso mudakhala chitsanzo kwa okhulupirira onse a ku Masedoniya ndi a ku Akaiya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kotero kuti munayamba kukhala inu chitsanzo kwa onse akukhulupirira m'Masedoniya ndi m'Akaya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo potero munakhala chitsanzo kwa abale onse a ku Makedoniya ndi Akaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kotero kuti munayamba kukhala inu citsanzo kwa onse akukhulupira m'Makedoniya ndi m'Akaya.