1 Thessalonians 2:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Abale, inu nomwe mukudziŵa kuti kucheza kuja tidadzacheza kwanuku, kunali kwaphindu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti, abale, mudziwa nokha malowedwe athu a kwa inu, kuti sanakhala opanda pake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abale, mukudziwa kuti kudzacheza kwathu kwa inu sikunali kosapindulitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti, abale, mudziwa nokha malowedwe athu a kwa inu, kuti sanakhala opanda pace;