1 Thessalonians 2:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja mukudziŵa kuti, tinkasamala aliyense mwa inu monga momwe amachitira bambo ndi ana ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
monga mudziwa kuti tinachitira yense wa inu pa yekha, monga atate achitira ana ake a iye yekha,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga mudziwa kuti ife tinkasamala aliyense wa inu monga abambo amasamalira ana ake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
monga mudziwa kuti tinacitira yense wa inu pa yekha, monga atate acitira ana ace a iye yekha, ndi kukudandaulirani, ndi kukusangalatsani ndi kucita umboni,