1 Thessalonians 2:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ayudawo ndi amene adapha Ambuye Yesu ndi aneneri akale, ndipo adatizunza ifenso kwambiri. Ameneŵa sakondweretsa Mulungu konse, ndipo amadana ndi anthu onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amene adaphanso Ambuye Yesu, ndi aneneri, natilondalonda ife, ndipo sakondweretsa Mulungu, natsutsana nao anthu onse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
amene anapha Ambuye Yesu ndi aneneri ndipo anatithamangitsanso ife. Iwo sakondweretsa Mulungu ndipo amadana ndi anthu onse
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
amene adaphanso Ambuye Yesu, ndi aneneri, natilondalonda ife, ndipo sakondweretsa Mulungu, natsutsana nao anthu onse;