1 Thessalonians 2:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti zimene timalalika sitizilalika chifukwa chofuna kuphunzitsa zonama, kapena kuganiza zoipa, kapena kufuna kunyenga anthu ai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti kudandaulira kwathu sikuchokera kukusochera, kapena kuchidetso, kapena m'chinyengo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti kulalikira kumene tikuchita, sitikuchita ndi maganizo olakwika kapena zolinga zoyipa, kapenanso kufuna kukunamizani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti kudandaulira kwathu sikucokera kukusocera, kapena kucidetso, kapena m'dnyengo;