1 Thessalonians 2:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sitinkafunanso ulemu wochokera kwa anthu, kapena kwa inu, kapena kwa ena, ngakhale kunali kotheka kukulamulani kuti mutithandize, popeza kuti ndife atumwi a Khristu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kapena sitinakhala ofuna ulemerero wa kwa anthu, kapena kwa inu, kapena kwa ena, tingakhale tinali nayo mphamvu yakukulemetsani monga atumwi a Khristu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ife sitinafune kutamidwa ndi anthu, kapena ndi inu, kapena wina aliyense mwa inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kapena sitinakhala ofuna ulemerero wa kwa anthu, kapena kwa inu, kapena kwa ena, tingakhale tinali nayo mphamvu yakukulemetsanl monga atumwi a Kristu.