1 Thessalonians 2:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma tidakhala ofatsa pakati panu ngati mai wosamalira ana ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Komatu tinakhala ofatsa pakati pa inu, monga m'mene mlezi afukata ana ake a iye yekha;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati atumwi a Khristu tikanatha kukhala cholemetsa kwa inu, mʼmalo mwake tinali ngati ana aangʼono pakati panu. Monga mmene amayi amasamalira ana awo angʼono,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Komatu tinakhala ofat sa pakati pa inu, monga m'mene mlezi afukata ana ace a iye yekha;