1 Thessalonians 3:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nanga tingathe bwanji kuyamika Mulungu mokwanira chifukwa cha inu, poona chimwemwe chonse chimene tili nacho pamaso pa Mulungu wathu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti tikhoza kubwezera kwa Mulungu chiyamiko chanji chifukwa cha inu, pa chimwemwe chonse tikondwera nacho mwa inu pamaso pa Mulungu wathu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tingathe bwanji kuyamika Mulungu mokwanira poona chimwemwe chonse chimene tili nacho pamaso pa Mulungu wathu chifukwa cha inu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti tikhoza kubwezera kwa Mulungu ciyamiko canji cifukwa ca inu, pa cimwemwe conse tikondwera naco mwa inu pamaso pa Mulungu wathu;