1 Thessalonians 4:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo mumakondana nawodi abale onse a m'dziko lonse la Masedoniya. Koma tikukupemphani abale, kuti muchite zimenezi koposa kale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakutinso munawachitira ichi abale onse a m'Masedoniya lonse. Koma tikudandaulirani, abale, muchulukireko koposa,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo kunena zoona, mumakonda abale onse a mʼbanja la Mulungu a ku Makedoniya. Komabe, abale tikukulimbikitsani kuti muzichita zimenezi koposa kale.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakutinso munawacitira ici abale onse a m'Makedoniya lonse. Koma tikudandaulirani, abale, mueurukireko koposa,