1 Thessalonians 5:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komatu abale, za nthaŵi ndi nyengo yake yodzachitika zimenezi, nkosafunikira kuti ndichite kukulemberani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma za nthawizo ndi nyengozo, abale, sikufunika kuti tidzakulemberani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono abale, za nthawi ndi nyengo yake nʼkosafunikira kuti tikulembereni,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma za nthawizo ndi nyengozo, abale, sikufunika kuti tidzakulemberani,