1 Thessalonians 5:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake muzilimbitsana mtima ndi kumathandizana, monga momwe mukuchitiramu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwa ichi chenjezanani, ndipo mangiriranani wina ndi mnzake, monganso mumachita.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho limbikitsanani wina ndi mnzake ndi kuthandizana kukula mu mzimu, monga momwe mukuchitira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwa ici cenjezanani, ndipo mangiriranani wina ndi mnzace, monganso mumacita,