1 Thessalonians 5:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma inu abale, simuli m'chimbulimbuli kuti tsikulo nkukudzidzimutsani ngati mbala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma inu, abale, simuli mumdima, kuti tsikulo likakugwereni monga mbala;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma inu abale, simuli mu mdima kuti tsiku limeneli lidzakudzidzimutseni ngati mbala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kama inu, abale, simuli mumdima, kuti tsikulo likakugwereni monga mbala;