1 Thessalonians 5:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake tsono tisagone tulo monga momwe amachitira anthu ena, ife tikhale maso, tikhale osaledzera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa chake tsono tisagone monga otsalawo, komatu tidikire, ndipo tisaledzere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chomwecho tsono, tisafanane ndi ena amene akugona koma tikhale maso ndi odzisunga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cifukwa cace tsono tisagone monga otsalawo, komatu tidikire, ndipo tisaledzere,