1 Timothy 1:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tikudziŵa kuti Malamulo ngabwino, malinga nkuŵagwiritsa ntchito moyenera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mudziwa kuti lamulo ndi labwino, ngati munthu achita nalo monga mwa lamulo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tikudziwa kuti Malamulo ndi abwino ngati munthu awagwiritsa ntchito bwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mudziwa kuti lamulo ndi labwino, ngati munthu acita nalo monga mwa lamulo,