1 Timothy 3:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene ndikukulembera zimenezi, ndikuyembekeza kudzafika kwanuko posachedwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Izi ndikulembera ndi kuyembekeza kudza kwa iwe posachedwa, koma ngati ndichedwa,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale ndili ndi chiyembekezo choti ndifika komweko posachedwapa, ndikukulemberani malangizo awa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Izi ndikulembera ndi kuyembekeza kudza kwa iwe posacedwa, koma ngati ndicedwa,