1 Timothy 4:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mpaka pamene ndidzabwere, uchite khama kuŵerengera anthu mau a Mulungu, kuŵalalikira ndi kuŵaphunzitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kufikira ndidza ine, usamalire kuwerenga, kuchenjeza, kulangiza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mpaka nditabwera, udzipereke powerenga mawu a Mulungu kwa anthu, kulalikira ndi kuphunzitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kufikira ndidza ine, usamalire kuwerenga, kucenjeza, kulangiza.