1 Timothy 4:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Udziyang'anire bwino wekha, ndi kusamala zimene umaphunzitsa. Ulimbikire kutero, chifukwa pakuchita zimenezi udzadzipulumutsa iwe wemwe, ndiponso anthu amene amamva mau ako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Udzipenyerere wekha, ndi chiphunzitsocho. Uzikhala mu izi; pakuti pochita ichi udzadzipulumutsa iwe wekha ndi iwo akumva iwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Samala kwambiri moyo wako ndi ziphunzitso zako. Uzichitabe zimenezi chifukwa ukatero, udzadzipulumutsa ndiponso udzapulumutsa okumvetsera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Udzipenyerere wekha, ndi ciphunzitsoco. Uzikhala muizi; pakuti pocita ici udzadzipulumutsa iwe wekha ndi iwo akumva iwe.