1 Timothy 5:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mai wamasiye amene amangodzisangalatsa ndi zapansipano, ameneyo wafa kale ngakhale akali moyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iye wakutsata zomkondweretsa, adafa pokhala ali ndi moyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mkazi wamasiye amene amangokhalira kuchita zosangalatsa moyo wake, wafa kale ngakhale akanali ndi moyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iye wakutsata zomkondweretsa, adafa pokhala ali ndi moyo,