1 Timothy 6:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Uŵalamule kuti azichita zabwino, kuti azikhala olemera pa ntchito zabwino, oolowa manja, ndi okonda kugaŵana zinthu zao ndi anzao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti achite zabwino, nachuluke ndi ntchito zabwino, nakondwere kugawira ena, nayanjane;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uwalamule kuti azichita zabwino, kuti azikhala olemera pa ntchito zabwino, owolowamanja ndi okonda kugawana zinthu zawo ndi anzawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti acite zabwino, naeuruke ndi nchito zabwino, nakondwere kugawira ena, nayanjane;