1 Timothy 6:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakutero adzadziwunjikira chuma chokoma ndi chokhalitsa chimene chidzaŵathandize kutsogoloko, kuti akalandire moyo umene uli moyo weniweni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nadzikundikire okha maziko okoma ku nyengo ikudzayi, kuti akagwire moyo weniweniwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Potero adzadziwunjikira chuma chokhalitsa ngati maziko okhazikika a nthawi zakutsogolo, kuti akalandire moyo, umene ndi moyo weniweni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nadzikundikire okha maziko okoma ku nyengo ikudzayi, kuti akagwire moyo weni weniwo.