1 Timothy 6:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ena, chifukwa chovomereza nzeru zotere, adasokera nkutaya chikhulupiriro chao. Mulungu akukomere mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chimene ena pochivomereza adalakwa ndi kutaya chikhulupiriro. Chisomo chikhale nanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu ena chifukwa chovomereza nzeru zotere, asochera nʼkutaya chikhulupiriro chawo. Chisomo chikhale nawe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cimene ena pocibvomereza 1 adalakwa ndi kutaya cikhulupiriro. Cisomo cikhale nanu.