1 Timothy 6:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ngati tili ndi chakudya ndi zovala, zimenezi zitikwanire.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma pokhala nazo zakudya ndi zofunda, zimene zitikwanire.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati tili ndi chakudya ndi zovala, zimenezi zitikwanire.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma pokhala nazo zakudya ndizopfunda, zimenezi zitikwanire.