2 Chronicles 10:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Rehobowamu adakhala akulamulirabe Aisraele enawo okhala m'mizinda ya ku Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma za ana a Israele okhala m'midzi ya Yuda, Rehobowamu anakhalabe mfumu yao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Rehobowamu anakhala akulamulirabe Aisraeli amene amakhala mʼmizinda ya Yuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma za ana a Israyeli okhala m'midzi ya Yuda, Rehabiamu anakhalabe mfumu yao.