2 Chronicles 10:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu adakamuitana. Choncho Yerobowamu pamodzi ndi Aisraele onse, adadza kwa Rehobowamu namuuza kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatuma munthu kukamuitana, nadza Yerobowamu ndi Aisraele onse, nalankhula ndi Rehobowamu, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero anthu anakayitana Yeroboamu ndipo iye ndi Aisraeli onse anapita kwa Rehobowamu ndi kumuwuza kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatuma munthu kukamuitana, nadza Yerobiamu ndi Aisrayeli onse, nalankhula ndi Rehabiamu, ndi kuti,